1 Mbiri 27:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo woyang'anira cuma ca mfumu ndiye Azimaveti mwana wa Adiyeli, ndi woyang'anira wa cuma ca m'minda, m'mizinda ndi m'miraga, ndi nyumba za nsanja, ndiye Yonatani mwana wa Uziya;

1 Mbiri 27

1 Mbiri 27:23-31