1 Mbiri 27:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Yoabu mwana wa Zeruya anayamba kuwerenga, koma sanatsiriza; ndi mkwiyo unagwera Israyeli cifukwa ca ici, ndipo ciwerengo cao sicinalembedwa m'buku la mbiri ya mfumu Davide.

1 Mbiri 27

1 Mbiri 27:14-34