1 Mbiri 23:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

A iwowa zikwi makumi awiri mphambu zinai anayang'anira nchito ya nyumba ya Yehova, ndi zikwi zisanu ndi cimodzi ndiwo akapitao ndi oweruza,

1 Mbiri 23

1 Mbiri 23:1-6