1 Mbiri 23:31 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndi kupereka nsembe zopsereza zonse kwa Yehova, za masabata, za pokhala mwezi, za nyengo zoikika, kuwerenga kwace monga mwa lemba lace, kosalekeza pamaso pa Yehova;

1 Mbiri 23

1 Mbiri 23:27-32