1 Mbiri 21:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma sanawerenga Alevi ndi Abenjamini pakati pao; pakuti mau a mfumu anamnyansira Yoabu.

1 Mbiri 21

1 Mbiri 21:4-7