1 Mbiri 21:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yoabu anapereka kwa Davide ciwerengo ca anthu owerengedwa. Ndipo Aisrayeli onse anali zikwi mazana khumi ndi limodzi osolola lupanga, ndi Yuda anali zikwi mazana anai mphambu makumi asanu ndi awiri akusolola lupanga,

1 Mbiri 21

1 Mbiri 21:1-12