1 Mbiri 2:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndi Gesuri ndi Aramu analanda midzi ya Yairi, pamodzi ndi Kenati ndi miraga yace; ndiyo midzi makumi asanu ndi limodzi. Iwo onse ndiwo ana a Makiri atate wa Gileadi.

1 Mbiri 2

1 Mbiri 2:20-25