1 Mbiri 18:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anaika asilikari a boma m'Edomu; ndi Aedomu onse anasanduka anthu a Davide. Ndipo Yehova anasunga Davide kuli konse anamukako.

1 Mbiri 18

1 Mbiri 18:12-17