1 Mbiri 17:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Inde likhazikike dzina lanu, likulitsidwe kosalekeza, ndi kuti, Yehova wa makamu ndiye Mulungu wa Israyeli; akhalira Israyeli Mulungu; ndi nyumba ya Davide mtumiki wanu ikhazikika pamaso panu.

1 Mbiri 17

1 Mbiri 17:16-27