1 Mbiri 15:29 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo polowa likasa la cipangano la Yehova m'mudzi wa Davide, Mikala mwana wamkazi wa Sauli anasuzumira pazenera, naona mfumu Davide alikutumphatumpha ndi kusewera; ndipo anampeputsa mumtima mwace.

1 Mbiri 15

1 Mbiri 15:25-29