1 Mbiri 15:28 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Momwemo Aisrayeli onse anakwera nalo likasa la cipangano la Yehova ndi kupfuula, ndi kumveka kwa lipenga, ndi mphalasa, ndi nsanje zomveketsa, ndi zisakasa, ndi azeze.

1 Mbiri 15

1 Mbiri 15:18-29