1 Mbiri 15:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti, cifukwa ca kusalinyamula inu poyamba paja, Yehova Mulungu wathu anacita cotipasula, popeza sitinamfunafuma Iye monga mwa ciweruzo.

1 Mbiri 15

1 Mbiri 15:12-16