1 Mbiri 15:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Inu ndinu akuru a nyumba za makolo a Alevi, mudzipatule inu ndi abale anu omwe, kuti mukatenge ndi kukwera nalo likasa la Yehova Mulungu wa Israyeli ku malo ndalikonzera.

1 Mbiri 15

1 Mbiri 15:7-20