1 Mbiri 14:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Davide anazindikira kuti Yehova adamkhazikitsa mfumu ya Israyeli; pakuti ufumu wace unakwezekadi, cifukwa ca anthu ace Israyeli.

1 Mbiri 14

1 Mbiri 14:1-5