1 Mbiri 14:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Hiramu mfumu ya Turo anatumiza mithenga kwa Davide, ndi mikungudza, ndi amisiri omanga miyala, ndi amatabwa, kuti ammangire nyumba.

1 Mbiri 14

1 Mbiri 14:1-3