1 Mbiri 12:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pomuka iye ku Zikilaga anapambukira kwa iye a Manase: Adina, ndi Yozabadi, ndi Yedyaeli, ndi Mikaeli, ndi Yozabadi, ndi Elihu, ndi Ziletai, akuru a zikwi a ku Manase.

1 Mbiri 12

1 Mbiri 12:11-23