1 Mbiri 12:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Anakoka mauta; naponya miyala, naponya mibvi ndi uta ndi dzanja lamanja ndi lamanzere lomwe; ndiwo a abale ace a Sauli, Abenjamini.

1 Mbiri 12

1 Mbiri 12:1-10