41. Uriya Mhiti, Zabadi mwana wa Alai,
42. Adina mwana wa Siza Mrubeni mkuru wa Arubeni, ndi makumi atatu pamodzi naye,
43. Hanani mwana wa Maaka, ndi Yosafati Mmitini,
44. Uziya M-asterati, Sama ndi Yeieli ana a Hotamu wa ku Aroeri,
45. Yedyaeli mwana wa Simri, ndi Yoha mbale wace Mtizi,
46. Elieli Mmahavi, ndi Yeribai ndi Yosaviya ana a Elinaamu, ndi Itima Mmoabu,
47. Elieli, ndi Obedi, ndi Yasiyeli Mmezobai.