1 Mbiri 11:38-43 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

38. Yoeli mbale wa Natani, Mibari mwana wa Hagiri,

39. Zeleki M-amoni, Naharai Mberoti wonyamula zida za Yoabu mwana wa Zeruya,

40. Ira M-itiri, Garebi M-itiri,

41. Uriya Mhiti, Zabadi mwana wa Alai,

42. Adina mwana wa Siza Mrubeni mkuru wa Arubeni, ndi makumi atatu pamodzi naye,

43. Hanani mwana wa Maaka, ndi Yosafati Mmitini,

1 Mbiri 11