1 Mbiri 11:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Anaphanso M-aigupto munthu wamkuru, msinkhu wace mikono isanu, ndi m'dzanja la M-aigupto munali mkondo ngati mtanda woombera nsaru; ndipo anamtsikira ndi ndodo, nakwatula mkondo m'dzanja la M-aigupto, namupha ndi mkondo wace womwe.

1 Mbiri 11

1 Mbiri 11:13-30