1 Mafumu 8:56 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Wolemekezeka ndi Yehova amene anapumulitsa anthu ace Aisrayeli, monga mwa zonse analonjezazo; sanatayika mau amodzi a mau ace onse abwino, amene analankhula ndi dzanja la Mose mtumiki wace.

1 Mafumu 8

1 Mafumu 8:52-60