1 Mafumu 8:53 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Popeza Inu munawapatula pa anthu onse a pa dziko lapansi akhale colowa canu, monga munanena ndi dzanja la Mose mtumiki wanu, pamene munaturutsa makolo athu m'Aigupto, Yehova Mulungu Inu.

1 Mafumu 8

1 Mafumu 8:43-55