1 Mafumu 8:52 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

kuti maso anu akatsegukire pembedzero la kapolo wanu ndi pembedzero la anthu anu Aisrayeli, kuwamveram'menemonseakapfuula kwa Inu.

1 Mafumu 8

1 Mafumu 8:44-58