1 Mafumu 7:41 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nsanamira ziwirizo, ndi mbale za mitu inali pamwamba pa nsanamira ziwirizo, ndi maukonde awiri ophimbira mbale ziwiri za mitu inali pamwamba pa nsanamirazo,

1 Mafumu 7

1 Mafumu 7:35-46