1 Mafumu 7:36 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo m'mapanthi mwa mbano zace ndi pa matsekerezo ace analemba ngati akerubi ndi mikango ndi migwalangwa, monga mwa malo ace a zonsezo, ndi zoyangayanga zozungulira.

1 Mafumu 7

1 Mafumu 7:30-46