1 Mafumu 7:35 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pamwamba pa phaka panali khoma lozunguniza, msinkhu wace nusu ya mkono; ndi pamwamba pa phaka panali mbano zace ndi matsekerezo a phaka lomwelo.

1 Mafumu 7

1 Mafumu 7:31-42