1 Mafumu 5:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma tsopano Yehova Mulungu wanga wandipumulitsa ku mbali zonse; palibe wotsutsana nane, kapena coipa condigwera.

1 Mafumu 5

1 Mafumu 5:1-7