1 Mafumu 5:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mudziwa inu kuti atate wanga Davide sanathe kumangira dzina la Yehova Mulungu wace nyumba, cifukwa ca nkhondo zakumzinga konseko, mpaka atawaika Yehova pansi pa mapazi ace.

1 Mafumu 5

1 Mafumu 5:1-10