1 Mafumu 22:46-48 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

46. Ndipo anacotsa m'dziko anyamata onyansa aja adatsalira masiku a atate wace Asa.

47. Ndipo m'Edomu munalibe mfumu, koma kazembe wa mfumu.

48. Yehosafati anamanga zombo za ku Tarsisi kukatenga golidi ku Ofiri; koma sizinamuka, popeza zinaphwanyika pa Ezioni Geberi.

1 Mafumu 22