1 Mafumu 21:29 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Waona umo wadzicepetsera Ahabu pamaso panga? Popeza adzicepetsa pamaso panga, sindidzafikitsa coipa cimeneci akali moyo iye; koma m'masiku a mwana wace ndidzacifikitsa pa nyumba yace.

1 Mafumu 21

1 Mafumu 21:26-29