1 Mafumu 22:40 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Ahabu anagona ndi makolo ace; ndi Ahaziya mwana wace anakhala mfumu m'malo mwace.

1 Mafumu 22

1 Mafumu 22:35-46