1 Mafumu 22:39 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Tsono macitidwe ena a Ahabu, ndi zonse adazicita, ndi nyumba ya minyanga adaimanga, ndi midzi yonse adaimanga, kodi sizilembedwa m'buku la macitidwe a mafumu a Israyeli?

1 Mafumu 22

1 Mafumu 22:36-44