1 Mafumu 22:31 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Tsono mfumu ya Aramu idalamulira akapitao makumi atatu mphambu ziwiri za magareta ace, niti, Musaponyana ndi anthu ang'ono kapena akuru, koma ndi mfumu ya Israyeli yokha.

1 Mafumu 22

1 Mafumu 22:23-39