1 Mafumu 22:30 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mfumu ya Israyeli inanena ndi Yehosafati, Ine ndidzadzizimbaitsa, ndi kulawa kunkhondo, koma bvala iwe zobvala zako zacifumu. Ndipo mfumu ya Israyeli inadzizimbaitsa, nilowa kunkhondo.

1 Mafumu 22

1 Mafumu 22:29-40