1 Mafumu 20:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anyamata a mfumu ya Aramu anati kwa iye, Milungu yao nja kumapiri, ndimo m'mene atilakira; koma tikaponyana nao kucidikha, zedi tidzaposa mphamvu.

1 Mafumu 20

1 Mafumu 20:20-33