1 Mafumu 20:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Tsono mfumu ya Israyeli inaturuka, nikantha apakavalo ndi apamagareta, nawapha Aaramuwo maphedwe akuru.

1 Mafumu 20

1 Mafumu 20:14-23