1 Mafumu 19:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo iye ataona cimeneci, ananyamuka, nathawa kupulumutsa moyo, nafika ku Beereseba wa ku Yuda, nasiya mnyamata wace pamenepo.

1 Mafumu 19

1 Mafumu 19:2-4