1 Mafumu 19:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Tsono Yezebeli anatuma mthenga kwa Eliya, wakuti, Milungu indilange nionjezepo, ngati sindilinganiza moyo wako ndi moyo wa mmodzi wa iwowo mawa nthawi yomwe yino.

1 Mafumu 19

1 Mafumu 19:1-12