1 Mafumu 18:31 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Eliya anatenga miyala khumi ndi iwiri, monga mwa ciwerengo ca mafuko a ana a Yakobo, amene mau a Yehova adamfikira, kuti, Dzina lako ndi Israyeli.

1 Mafumu 18

1 Mafumu 18:28-34