1 Mafumu 18:30 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo Eliya ananena ndi anthu onse, Senderani kwa ine; ndipo onse anasendera kwa iye. Iye nakonza guwa la nsembe la Yehova lidagumukalo.

1 Mafumu 18

1 Mafumu 18:26-35