1 Mafumu 16:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Caka ca makumi atatu ndi cimodzi ca Asa mfumu ya Yuda, Omri anayamba kukhala mfumu ya Israyeli, nakhala zaka khumi ndi ziwiri; ku Tiriza anali mfumu zaka zisanu ndi cimodzi.

1 Mafumu 16

1 Mafumu 16:21-25