1 Mafumu 13:31 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kunacitika, atamuika iye, ananena ndi ana ace, nati, Nkadzamwalira ine mudzandiike ine m'manda momwemo mwaikidwa munthu wa Mulunguyo, ikani mafupa anga pafupi ndi mafupa ace.

1 Mafumu 13

1 Mafumu 13:21-34