1 Mafumu 12:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Potero mfumu siinamvera anthuwo, pakuti kusintha uku kunacokera kwa Yehova, kuti akhazikitse mau ace amene Yehova ananenetsa Abiya wa ku Silo kwa Yerobiamu mwana wa Nebati.

1 Mafumu 12

1 Mafumu 12:7-22