1 Mafumu 12:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

nalankhula nao monga mwa uphungu wa acinyamata, nati, Atate wanga analemeretsa gori lanu, koma ine ndidzaonjezerapo pa gori lanu; atate wanga anakukwapulani ndi zikoti, koma ine ndidzakukwapulani ndi zinkhanira,

1 Mafumu 12

1 Mafumu 12:4-19