1 Mafumu 1:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Adoniya anapha nkhosa ndi ng'ombe ndi nyama zonona pamwala pa Zoheleti, uli pafupi ndi citsime ca Rogeli, naitana abale ace onse ana a mfumu, ndi anthu onse a Yuda anayamata a mfumu;

1 Mafumu 1

1 Mafumu 1:2-14