1 Mafumu 1:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma Zadoki wansembe, ndi Benaya mwana wace wa Yehoyada, ndi Natani mneneri, ndi Simeyi, ndi Reyi, ndi anthu amphamvu aja adali ndi Davide, sanali ndi Adoniya.

1 Mafumu 1

1 Mafumu 1:1-17