1 Atesalonika 4:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cotsalira tsono, abale, tikupemphani ndi kukudandaulirani mwa Ambuye Yesu, kuti, monga munalandira kwa ife mayendedwe okoma, muyenera kuyendanso ndi kukondweretsa Mulungu, monganso mumayenda, eurukani koposa momwemo.

1 Atesalonika 4

1 Atesalonika 4:1-4