1 Atesalonika 2:18-20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

18. cifukwa tinafuna kudza kwa inu, inedi Paulo ndatero kamodzi kapena kawiri; koma Satana anatiletsa.

19. Pakuti ciyembekezo cathu, kapena cimwemwe, kapena korona wakudzitamandira naye nciani? si ndinu nanga pamaso pa Ambuye wathu Yesu m'kufika kwace?

20. Pakuti inu ndinu ulemerero wathu ndi cimwemwe cathu.

1 Atesalonika 2