1 Atesalonika 2:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti ciyembekezo cathu, kapena cimwemwe, kapena korona wakudzitamandira naye nciani? si ndinu nanga pamaso pa Ambuye wathu Yesu m'kufika kwace?

1 Atesalonika 2

1 Atesalonika 2:18-20