1 Akorinto 14:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace, ngati Mpingo wonse akasonkhane pamodzi, ndi onse akalankhule malilime, ndipo akalowemo anthu osaphunzira kapena osakhulupira, kodi sadzanena kuti mwayaruka?

1 Akorinto 14

1 Akorinto 14:22-29